Nehemiya 7:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanawapeze.+ Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+
64 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanawapeze.+ Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+