Nehemiya 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abale ake a Adaya, atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ analipo 242. Ndiyeno panalinso Amasisai mwana wa Azareli. Azareli anali mwana wa Azai, Azai anali mwana wa Mesilemoti amene anali mwana wa Imeri.
13 Abale ake a Adaya, atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ analipo 242. Ndiyeno panalinso Amasisai mwana wa Azareli. Azareli anali mwana wa Azai, Azai anali mwana wa Mesilemoti amene anali mwana wa Imeri.