Nehemiya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthawi yonseyi ine sindinali mu Yerusalemu, pakuti m’chaka cha 32+ cha ulamuliro wa Aritasasita+ mfumu ya Babulo, ndinabwerera kwa mfumu. Patapita nthawi, ndinapempha mfumuyo kuti ndichoke.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:6 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 11
6 Nthawi yonseyi ine sindinali mu Yerusalemu, pakuti m’chaka cha 32+ cha ulamuliro wa Aritasasita+ mfumu ya Babulo, ndinabwerera kwa mfumu. Patapita nthawi, ndinapempha mfumuyo kuti ndichoke.+