-
Esitere 9:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno mfumu inauza Mfumukazi Esitere+ kuti: “Kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani+ Ayuda apha ndi kuwononga amuna 500 pamodzi ndi ana 10 a Hamani. Ndiye kuli bwanji nanga m’zigawo zina zonse+ za mfumu?+ Choncho, ukufuna kupempha chiyani? Chimene ukufunacho ndikupatsa.+ Ukufunanso chiyani china?+ Chimene ukufunacho chichitika.”
-