Esitere 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Esitere ataonekera pamaso pa mfumu, mfumuyo inalemba lamulo lakuti:+ “Chiwembu+ chake choipa chimene anakonzera Ayuda chimugwere iyeyo.”+ Choncho Hamani komanso ana ake anawapachika pamtengo.+
25 Koma Esitere ataonekera pamaso pa mfumu, mfumuyo inalemba lamulo lakuti:+ “Chiwembu+ chake choipa chimene anakonzera Ayuda chimugwere iyeyo.”+ Choncho Hamani komanso ana ake anawapachika pamtengo.+