Yobu 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Uyu ali mkati molankhula kunabwera munthu wina kudzanena kuti: “Moto wa Mulungu watsika kuchokera kumwamba,+ ndipo wayaka pakati pa nkhosa ndi abusa n’kupsereza nkhosazo ndi abusawo. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.” Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,11/15/1994, ptsa. 11-12
16 Uyu ali mkati molankhula kunabwera munthu wina kudzanena kuti: “Moto wa Mulungu watsika kuchokera kumwamba,+ ndipo wayaka pakati pa nkhosa ndi abusa n’kupsereza nkhosazo ndi abusawo. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.”