Yobu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kwa Iye amene amakola anzeru m’kuchenjera kwawo,+Iye amene amachititsa kuti malangizo a ochenjera abweretse chisokonezo.+
13 Kwa Iye amene amakola anzeru m’kuchenjera kwawo,+Iye amene amachititsa kuti malangizo a ochenjera abweretse chisokonezo.+