Yobu 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene moyo wake umathera,+Ndipo m’fumbimo mumamera zina.