Yobu 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mimba idzamuiwala, mphutsi zidzamumva kutsekemera pomuyamwa,+Ndipo iye sadzakumbukiridwanso.+Kupanda chilungamo kudzathyoledwa ngati mtengo.+
20 Mimba idzamuiwala, mphutsi zidzamumva kutsekemera pomuyamwa,+Ndipo iye sadzakumbukiridwanso.+Kupanda chilungamo kudzathyoledwa ngati mtengo.+