Yobu 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Mulungu samva kufuula kwa anthu olankhula zinthu zonama,+Ndipo Wamphamvuyonse sawaona.+