Yobu 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungutu ndi wamphamvu+ ndipo sadzakana munthu.Iye ali ndi mphamvu zazikulu zomvetsa zinthu.