Salimo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzadzikonzera zida za imfa,+Ndipo adzapanga mivi yake kukhala yoyaka moto walawilawi.+