Salimo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:6 Nsanja ya Olonda,1/15/1999, tsa. 20
6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+