Salimo 45:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Mtima wanga wagalamuka chifukwa cha nkhani yosangalatsa.+Ine ndikuti: “Nyimbo yangayi ikunena za mfumu.”+Lilime langa likhale ngati cholembera+ cha wokopera malemba waluso.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:1 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, ptsa. 3-43/1/1987, ptsa. 22-2310/15/1986, tsa. 29
45 Mtima wanga wagalamuka chifukwa cha nkhani yosangalatsa.+Ine ndikuti: “Nyimbo yangayi ikunena za mfumu.”+Lilime langa likhale ngati cholembera+ cha wokopera malemba waluso.+