Salimo 49:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe munthu wochokera kufumbi, ngakhale atakhala wolemekezeka, sangakhale ndi moyo mpaka kalekale.+Iye amangofanana ndi nyama zimene zaphedwa.+
12 Komabe munthu wochokera kufumbi, ngakhale atakhala wolemekezeka, sangakhale ndi moyo mpaka kalekale.+Iye amangofanana ndi nyama zimene zaphedwa.+