Salimo 60:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Inu Mulungu, mwatitaya, ndipo mwasokoneza magulu athu ankhondo,+Mwakwiya. Tiloleni tibwerere kwa inu.+
60 Inu Mulungu, mwatitaya, ndipo mwasokoneza magulu athu ankhondo,+Mwakwiya. Tiloleni tibwerere kwa inu.+