Salimo 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma tsopano mwatitaya ndi kutichititsa manyazi,+Simukuyenda ndi magulu athu ankhondo.+ Salimo 89:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma inu mwataya wodzozedwa wanu moti mukupitiriza kunyansidwa naye,+Ndipo mwamukwiyira.+