2 Samueli 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pita, ukauze Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndaika zilango zitatu pamaso pako.+ Sankha wekha chimodzi mwa zitatuzi chimene ukufuna kuti ndikuchitire.”’”+ Zekariya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+
12 “Pita, ukauze Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndaika zilango zitatu pamaso pako.+ Sankha wekha chimodzi mwa zitatuzi chimene ukufuna kuti ndikuchitire.”’”+
7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+