Salimo 60:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi thandizo la Mulungu, tidzalandira mphamvu,+Ndipo Mulungu adzapondereza adani athu.+