Salimo 78:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuti m’badwo wa m’tsogolo, ana amene adzabadwe m’tsogolo, adzadziwe zimenezi,+Kuti nawonso adzanyamuke ndi kusimbira ana awo.+
6 Kuti m’badwo wa m’tsogolo, ana amene adzabadwe m’tsogolo, adzadziwe zimenezi,+Kuti nawonso adzanyamuke ndi kusimbira ana awo.+