Salimo 71:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+ Salimo 102:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zimenezi zalembedwera m’badwo wam’tsogolo.+Ndipo anthu amene adzakhalapo m’tsogolo* adzatamanda Ya.+
18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+
18 Zimenezi zalembedwera m’badwo wam’tsogolo.+Ndipo anthu amene adzakhalapo m’tsogolo* adzatamanda Ya.+