Salimo 80:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onani muzu umene dzanja lanu lamanja linabzala.+Muonenso mwana wanu amene munamulimbitsa kuti inu mulemekezeke.+
15 Onani muzu umene dzanja lanu lamanja linabzala.+Muonenso mwana wanu amene munamulimbitsa kuti inu mulemekezeke.+