Salimo 80:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu Yehova Mulungu wa makamu, tibwezeretseni mwakale.+Walitsani nkhope yanu kuti tipulumutsidwe.+