Salimo 83:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mofanana ndi moto wotentha nkhalango,+Ndiponso malawi a moto woyaka m’mapiri,+