Yeremiya 46:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Adaniwo ndi ochuluka kwambiri kuposa dzombe+ ndipo ndi osawerengeka, moti adzadula nkhalango+ yake chifukwa sangathe kudutsamo,’ watero Yehova. Malaki 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ng’anjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi.+ Tsiku limene likubweralo lidzawanyeketsa moti pa iwo sipadzatsala mizu kapena nthambi,”+ watero Yehova wa makamu.
23 Adaniwo ndi ochuluka kwambiri kuposa dzombe+ ndipo ndi osawerengeka, moti adzadula nkhalango+ yake chifukwa sangathe kudutsamo,’ watero Yehova.
4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ng’anjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi.+ Tsiku limene likubweralo lidzawanyeketsa moti pa iwo sipadzatsala mizu kapena nthambi,”+ watero Yehova wa makamu.