Salimo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mudzawakhalitsa ngati oponyedwa mung’anjo yamoto pa nthawi ya kuonekera kwanu.+Yehova adzawameza mu mkwiyo wake, ndipo moto udzawanyeketsa.+ Zefaniya 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lamulo lisanayambe kugwira ntchito,+ tsiku lisanadutse ngati mankhusu,* mkwiyo woyaka moto wa Yehova usanakugwereni anthu inu,+ tsiku la mkwiyo wa Yehova lisanakufikireni,+ Mateyu 13:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako adzawaponya m’ng’anjo yamoto.+ Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.+ 2 Atesalonika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+ 2 Petulo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mwa mawu amodzimodziwo, kumwamba+ kumene kulipo panopa limodzi ndi dziko lapansi,+ azisungira moto+ m’tsiku lachiweruzo+ ndi chiwonongeko cha anthu osaopa Mulungu.+
9 Mudzawakhalitsa ngati oponyedwa mung’anjo yamoto pa nthawi ya kuonekera kwanu.+Yehova adzawameza mu mkwiyo wake, ndipo moto udzawanyeketsa.+
2 Lamulo lisanayambe kugwira ntchito,+ tsiku lisanadutse ngati mankhusu,* mkwiyo woyaka moto wa Yehova usanakugwereni anthu inu,+ tsiku la mkwiyo wa Yehova lisanakufikireni,+
8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+
7 Ndipo mwa mawu amodzimodziwo, kumwamba+ kumene kulipo panopa limodzi ndi dziko lapansi,+ azisungira moto+ m’tsiku lachiweruzo+ ndi chiwonongeko cha anthu osaopa Mulungu.+