Salimo 85:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zakumana.+Chilungamo ndi mtendere zapsompsonana.+