Salimo 86:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima.+Patsani mtumiki wanu mphamvu,+Ndipo pulumutsani mwana wa kapolo wanu wamkazi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:16 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, ptsa. 26-2712/15/1992, ptsa. 17-19
16 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima.+Patsani mtumiki wanu mphamvu,+Ndipo pulumutsani mwana wa kapolo wanu wamkazi.+