Salimo 88:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa lidzafika kwa inu.+Tcherani khutu lanu kuti mumve kuchonderera kwanga.+