1 Mafumu 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mumve pemphero lopempha chifundo+ la mtumiki wanu ndi la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayang’ana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ ndipo mumve n’kukhululuka.+ Salimo 79:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mverani kuusa moyo kwa mkaidi.+Anthu opita kukaphedwa muwateteze ndi dzanja lanu lamphamvu.+
30 Mumve pemphero lopempha chifundo+ la mtumiki wanu ndi la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayang’ana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ ndipo mumve n’kukhululuka.+