Salimo 88:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ine ndakumana ndi masoka ochuluka,+Ndipo moyo wanga wayandikira ku Manda.+