Salimo 103:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adzapitiriza kuchita zimenezi kwa anthu osunga pangano lake,+Ndi kwa anthu okumbukira malamulo ake ndi kuwatsatira.+
18 Adzapitiriza kuchita zimenezi kwa anthu osunga pangano lake,+Ndi kwa anthu okumbukira malamulo ake ndi kuwatsatira.+