Salimo 104:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Dzuwa likayamba kuwala+ zimachoka,Ndipo zimakagona m’malo awo obisalamo.