2 Samueli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+ Nahumu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda ako ali ngati dzombe ndipo akapitawo ako olemba anthu usilikali ali ngati gulu la dzombe. Pa tsiku lozizira limabisala m’makoma. Dzuwa likawala, dzombelo limauluka ndi kuthawira kutali ndipo silidziwika kuti lili kuti.+
4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+
17 Alonda ako ali ngati dzombe ndipo akapitawo ako olemba anthu usilikali ali ngati gulu la dzombe. Pa tsiku lozizira limabisala m’makoma. Dzuwa likawala, dzombelo limauluka ndi kuthawira kutali ndipo silidziwika kuti lili kuti.+