Salimo 105:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anamuika kukhala mkulu woyang’anira banja lake,+Komanso wolamulira chuma chake chonse.+