Salimo 105:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 M’dziko lawo munadzaza achule,+Chimodzimodzinso m’zipinda za mafumu awo.