Salimo 107:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+
19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+