Salimo 108:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Giliyadi+ ndi wanga ndipo Manase+ ndi wanganso.Efuraimu ndi malo otetezeka a mtsogoleri amene ine ndamuika.+Yuda ndi ndodo yanga ya mtsogoleri wa asilikali.+
8 Giliyadi+ ndi wanga ndipo Manase+ ndi wanganso.Efuraimu ndi malo otetezeka a mtsogoleri amene ine ndamuika.+Yuda ndi ndodo yanga ya mtsogoleri wa asilikali.+