Salimo 108:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mowabu+ ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu+ nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala+ chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+
9 Mowabu+ ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu+ nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala+ chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+