Salimo 109:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana ake azingoyendayenda ndithu,+Ndipo azipemphapempha.Azichoka m’mabwinja mmene akukhala, n’kupita kukafunafuna chakudya.+
10 Ana ake azingoyendayenda ndithu,+Ndipo azipemphapempha.Azichoka m’mabwinja mmene akukhala, n’kupita kukafunafuna chakudya.+