Salimo 109:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine ndiyenera kuchoka mofanana ndi chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa.+Ndakutumulidwa ngati dzombe. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 109:23 Nsanja ya Olonda,9/1/2006, tsa. 13
23 Ine ndiyenera kuchoka mofanana ndi chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa.+Ndakutumulidwa ngati dzombe.