1 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa. Yobu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amaphuka ngati duwa n’kuthotholedwa.+Amathawa ngati mthunzi+ ndipo sakhalaponso. Salimo 102:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masiku a moyo wanga ali ngati chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa,+Ndipo ndauma ngati udzu.+ Salimo 144:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amafanana ndi mpweya wotuluka m’mphuno.+Masiku ake ali ngati mthunzi wongodutsa.+ Yakobo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+
15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa.
11 Masiku a moyo wanga ali ngati chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa,+Ndipo ndauma ngati udzu.+
14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+