Salimo 115:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 115 Ife sitikuyenerera kalikonse, inu Yehova, ife sitikuyenerera kalikonse,+Koma dzina lanu ndi loyenera kulemekezedwa+Malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha, malinganso ndi choonadi chanu.+
115 Ife sitikuyenerera kalikonse, inu Yehova, ife sitikuyenerera kalikonse,+Koma dzina lanu ndi loyenera kulemekezedwa+Malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha, malinganso ndi choonadi chanu.+