Salimo 115:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Isiraeli, khulupirira Yehova.+Iye ndiye thandizo lako ndi chishango chako.+