Salimo 119:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ndidzapemphera kwa inu nditakweza manja anga chifukwa ndimakonda malamulo anu,+Ndipo ndidzasinkhasinkha malangizo anu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:48 Nsanja ya Olonda,10/1/2000, tsa. 151/15/1999, ptsa. 10-11
48 Ndidzapemphera kwa inu nditakweza manja anga chifukwa ndimakonda malamulo anu,+Ndipo ndidzasinkhasinkha malangizo anu.+