Salimo 119:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Ndayesetsa ndi mtima wanga wonse kuti mundiyanje.*+Ndikomereni mtima monga mwa mawu anu.+