Salimo 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ine ndidzayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+Ndiwomboleni+ ndi kundikomera mtima.+ Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+Pakuti ine ndathawira kwa inu.+Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+
11 Koma ine ndidzayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+Ndiwomboleni+ ndi kundikomera mtima.+
57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+Pakuti ine ndathawira kwa inu.+Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+