Salimo 119:92 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 92 Ndikanapanda kukonda chilamulo chanu,+Ndikanatheratu m’masautso anga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:92 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, tsa. 16