Salimo 119:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Mitima yawo yauma ngati mafuta oundana,+Koma ine ndimakonda chilamulo chanu.+ Salimo 119:77 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Ndisonyezeni chifundo chanu kuti ndikhalebe ndi moyo,+Pakuti ndimakonda chilamulo chanu.+ Salimo 119:143 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 143 Zowawa ndi zovuta zinandigwera.+Koma ndinakonda malamulo anu.+