Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+

      Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+

  • Salimo 103:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Monga mmene bambo amasonyezera chifundo kwa ana ake,+

      Yehova wasonyezanso chifundo kwa onse omuopa.+

  • Salimo 119:116
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 116 Inu Mulungu, ndithandizeni monga mwa mawu anu kuti ndikhalebe ndi moyo,+

      Ndipo musandichititse manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.+

  • Danieli 9:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mulungu wanga, tcherani khutu lanu kuti mumve.+ Tsegulani maso anu kuti muone kuwonongeka kwathu ndi kwa mzinda wotchedwa ndi dzina lanu.+ Ifeyo tikukuchondererani, osati chifukwa cha zochita zathu zolungama,+ koma chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+

  • Luka 1:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Chifundo chake chakhala pa amene amamuopa ku mibadwomibadwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena